Mwazi

The Very Best

Ukakhala iwe mphwanga
Usadzinamize uli ndi abale
Amakukonda uli ndi chuma
Ukasauka kukutaya
Amayiwala kuti mwazi ndi mwazi
Umawundana kuposa madzi

Iwe iwe mvera
Tchera tchera khutu
Ganiza ngati munthu